
Zomwe anena amalawi Ikakhala mbali ya ma President!!
Published on May 21, 2013 at 9:40 PM by FACE OF MALAWI
1. John Tembo sangayimire chifukwa m’manja mwake muli magazi
2. Atupele Muluzi ndi baby komanso mdala yyake inkasolola heve ili m’boma
3. Joyce Banda akumangomvera zili zonse anena a IMF
4. Thoko Banda ali ndi zaka 49 and single. Not good for a leader