
MIGHTY WANDERERS Vs CHIRADZULU UTD
Published on May 28, 2013 at 1:13 PM by FACE OF MALAWI
Mighty Wanderers kapena kuti THE NOMAS ilindi game lero pa 28/05/2013 nthawi ya 14:30hrs tiyeni tonse okonda Nyerere tikapeleke support yamphamvu kwatonse amenetiliku tali tingosegula MATINDI RADIO fm 91.9Mhz mchigawo chapakati ndimadela ozungulira timvele satanesatane wamasewelawa.
AGANYU CHANUPALIBE MUSAWEL