Dziko la Malawi ladandaula kazomwe dziko la Tanzania likufuna kuchita pogula Sitima zapamadzi zokwana 8 zomwe mwaizo ziwiri zikhala zikukankha mpalaula pa nyanja ya Malawi yomwe iwo akutinso ndiyawo, izi ndi zina zomwe akukambirana ku Tanzania Parliament kuyambira Friday.

Tanzania Ships on Lake Malawi Press Release by jkasalika1224