
NAMIBIA NATIONAL TEAM ILI M’DZIKO MUNO
Published on June 3, 2013 at 1:55 PM by FACE OF MALAWI
Team imeneyi yanenesa kuti flames izachinyidwa zigoli 5 mumphindi 10 zoyambilira pofuna kubwezela chipongwe chomwe anyamata aflames anaichita teamyi kwao,watero head coach wawo poyankhula ndi MBNV&I mumzinda waukulu wa Blantyre.