Bungwe la Asilamu m’dziko muno lapempha Ministry of Education kuti iyambitsenso phunziro la chisilamu (Islamic Studies) lomwe ana azitenga mokakamizidwa ku primary school and will be optional ku secondary.

Bungweli lapempha izi kutengera kuti ana amaphunzira religious studies ku Primary which focus mostly on Christianity and Bible Knowledge ku Secondary.