No featured image set for this post.
Man in Game Stores uniform, found dead near Kachere CCAP Church in Ndirande, Blantyre
Published on June 27, 2013 at 4:15 PM by FACE OF MALAWI
Bambo Kamzati omwe amagwira ntchito ku GAME Stores aphedwa dzulo pafupi ndi Kachere CCAP ku Ndirande.
Malinga ndi ma report amene MBNG yapeza, bamboyi amapita kwa chibwenzi chake ku Ndirande ko ngakhale kuti ndiwokwatira komanso ali ndi ana 5.
…
Mwini wake wa mkazi yo adamupeza bamboyu akuchezetsa ndipo adamemeza amzake omwe anayamba kuthamangitsa bambo Kamzati ndi zikwanje ndipo anayamba kuwakhapa mutu komanso pakhosi ndipo anataya magazi ochuluka.
Anyamata apanga zimenezi athawa koma tikuwuzani tsatane-tsatane akagwidwa poti a police akuwayang’ana.
Mkazi wa chibwenzi yu akusungidwa pa Ndirande Police Station!!