Malingana ndi ma report omwe akungotipeza kumene, dzina la mnyamata uja osawutsa anthu pakuwayamwa magazi ndi kugona akazi ayeni Nachipanti, nalo lili pa n’ndandanda wa akayidi omwe president Banda waakhululukila pokondwelera kuti dziko la Malawi, lakwanitsa zaka 45 lili paufulu wozilamulira.

Subscribe to our Youtube Channel: