1) DPP pankhani yachitetezo ndiye ndimbambande kusiyana ndi nthawi ino pomwe mbava zikungonyambitira kumva kukoma.

2) Munthawi ya DPP nkhani ya njala inali mbili ya dzana koma pano chimanga chayamba kale kusowa .

3) Professor Author Peter Muthalika ndiwophunzira kwabasi pomwe amayi ndi a form 4 ndinkuona dziko likuwavuta kuyendetsa.

4) Chipani cha DPP chimasanja mfundo zomwe zingathandize kutukula dziko lino pomwe PP ilibe mfundo iliyonse koma kutukwana m’misonkhano yawo.

5) Munthawi yaulamulilo wa DPP, misewu, Milatho, Mijigo, Misika yambiri inamangiwa ndi chitukuko chosiyanasiyana pomwe munthawi ya a mayi palibe chachitika basi uchembere wabwino ndikukweza mafumu.

6) Anthu ambiri omwe ankamusokoneza Bingu anakhamukila ku PP moti pano DPP yatsala ndi ma genius okhaokha monga achina Dausi ndigulu lawo omwe angathandize kutukula Malawi.

7) Munthawi ya DPP, anthu ovutika ankapeza mwayi wogula fetereza otsika mtengo pomwe PP ikumawachita chipongwe anthuwa powapatsa M’chenga ati kuwayeretsa m’maso.

8 ) Joyce Banda anadya matako agalu, nthawi yoyendetsa dziko alibe koma kunka nayendayenda ngati bakha.

9) Munthawi ya DPP, nkhani yoonera mayeso a ‘MANEB’ inali mbili ya make dzana pomwe nthawi ya a Mayi pansi paulamuliro wa PP, mayeso akuchita kupezeka pamsika ngati Bonya.

10) Anthu akufuna DPP ipitilize kumanga ma University aja anayamba kumanga Bingu aja( pajatu analonjeza 10, ndiye DPP ikalonjeza siyinama ayi mesa ina ndi ija ikuwakanika kutsekura amayi ija yothayitha)

ZIFUKWA KHUMI ZOMWE DPP ITALOWELENSO M'BOMA 2014!
1) DPP pankhani yachitetezo ndiye ndimbambande kusiyana ndi nthawi ino pomwe mbava zikungonyambitira kumva kukoma.
2) Munthawi ya DPP nkhani ya njala inali mbili ya dzana koma pano chimanga chayamba kale kusowa .
3) Professor Author Peter Muthalika ndiwophunzira kwabasi pomwe amayi ndi a form 4 ndinkuona dziko likuwavuta kuyendetsa.
4) Chipani cha DPP chimasanja mfundo zomwe zingathandize kutukula dziko lino pomwe PP ilibe mfundo iliyonse koma kutukwana m'misonkhano yawo.
5) Munthawi yaulamulilo wa DPP, misewu, Milatho, Mijigo, Misika yambiri inamangiwa ndi chitukuko chosiyanasiyana pomwe munthawi ya a mayi palibe chachitika basi uchembere wabwino ndikukweza mafumu.
6) Anthu ambiri omwe ankamusokoneza Bingu anakhamukila ku PP moti pano DPP yatsala ndi ma genius okhaokha monga achina Dausi ndigulu lawo omwe angathandize kutukula Malawi.
7) Munthawi ya DPP, anthu ovutika ankapeza mwayi wogula fetereza otsika mtengo pomwe PP ikumawachita chipongwe anthuwa powapatsa M'chenga ati kuwayeretsa m'maso.
8 ) Joyce Banda anadya matako agalu, nthawi yoyendetsa dziko alibe koma kunka nayendayenda ngati bakha.
9) Munthawi ya DPP, nkhani yoonera mayeso a 'MANEB' inali mbili ya make dzana pomwe nthawi ya a Mayi pansi paulamuliro wa PP, mayeso akuchita kupezeka pamsika ngati Bonya.