Woyimba otchuka wa ku Bangwe, Joe Gwaladi, waona malodza lero pamene wabeledwa njinga yake (bicycle) mu Limbe.

Gwaladi anayimitsa kabaza wakeyu panja pa Limbe Tavern mkulowa nkati mwa tavern kukashophetsa ma CD ake umo achitira nthawi zonse koma potuluka anangopeza njinga yasowa