ZIFUKWA 10 ZOMWE RASTA AMAKWATIRA MKAZI OKONGOLA.
1.Amakhala olimbika ntchito eg:Ras Peter Kansengwa,Jah works must be done.
2.Amakhala ophunzira,geli wise si nkhani chizungu chawo mcha standard saziluma polankhula.
3.Amakwanilisa chomwe wafuna eg: Blasto kukaponda ku Jamaica
4.Amabadwa ama looks EG:Anjiru,Prince Martin or Randy Martins ndipo amapitilira kuoneka bwino mma rocks(dreadrock)
4.Peace makers and freedom fighters
5.Friendly
6.Humble
7.Postive mind
8.Satengeka wamba
9.Amagwira ntchito ndi manja awo
10.Ndi anthu opatulika ndi opasa chidwi.
ZIFUKWA 10 ZOMWE MA YOO/NIGGA SAKWATIRA MZUNGU/MKAZI OKONGOLA
1.Ndi anthu amaluzi
/osauka amaika ka bible kakang’ono mthumba akazi aziti ndi wallet komanso amatha kudya bubblegum wa dzana anamumata pakhoma.
2.Amavala zikuluzikulu ngati azibibira ndi anthu oyenda ndi dziko.
3.Amabweleka zovala mkumapasana zikanga asakuone wavala kabwino mamawa akupeza kwanu.
4.Amavala zovala za alongo awo,msapato,baremuscle,blauzindi ma bokusa.
5.Sakhala ophumzira chizungu chomwe amadziwa iwo ndi yoo men,damn men.
6.Amaba ndalama kwawo kukamwera mowa.
7.Amapanga matama a chule omalumpha palibe dzenje.
8.Amadalira makolo awo,amakondanso ngongole ngakhale ndebvu amametesa pa ngongole.
9.Satha ndeu chifukwa zomwe amavala mzikuluzikulu sangathe kuponyako
10.Ma looks alibe amachita kukokela poika mohoku,kudula timizele,kuika ma tatoo,kukhwefula, kulankhula slang etc.
No comments! Be the first commenter?