
2 pigeons per family
Published on July 22, 2013 at 10:28 PM by FACE OF MALAWI
President Joyce Banda wati tsopano ayamba kugawa ‘nkhunda’ kuti anthu adziweta pantchito yake yofuna kuthana ndi umphawi m’dziko muno. Malingana ndi Joyce, banja lomwe lizisankhidwa, lizilandila nkhunda ziwiri (yayimuna ndi yayikazi) ndipo programme yi idzitchedwa ‘2 pigeons per family’