
DC wa boma la Mulanje yowopsyeza anthu ogwira ntchito ku District Council
Published on September 5, 2013 at 10:41 AM by FACE OF MALAWI
Iyi ndi kalata yomwe analemba DC wa boma la Mulanje yowopsyeza anthu ogwira ntchito ku District Council kuti akafuna kugwira ntchito za chitukuko aziyamba adziwitsa kaye Brown Mpinganjira yemwe ndi nduna yowona za chitukuko chamadzi yemwenso akufuna kuzayimila ngati phungu mdera lake ku Mulanje-ko.
DC anawopsyeza aliyense yemwe satsatila lamulori kuti zikazamuvuta zake zimenezo asazati sanamve.