__________________________

.
1- Anopheles Mosquito: awa ndi akazi omukolola mwamuna moipa. Palibe chomwe amamuthandiza koma harvesting basi.
.
2- Siku Transport: awa ndi akazi ogona ndi mwamuna aliyense, pena paliponse, nthawi iliyonse ngakhale popanda chikondi. Iwo bola ndalama. Amatha kugona ndi bambo, ana ake awiri ndi
wantchitonso pompo.
.
3- Chitute: awa ndi akazi omatuta katundu wapakhomo mwanseri
ndikumakabisa kwawo, ati kuopa banja litatha mwadzidzidzi.
.
4- Pharmacy: mkazi wokhulupilira zitsamba muchina chili chonse. Asamve kuti mwamuna wake kuntchito kwabwera woman nthawi yomweyo wakumudzi, akuti kukalimbitsa banja.
.
5- MRA: kuwerengera salary yamwamuna movuta muja. Mwamuna asayerekeze kumwera Fanta pochoka kolandira, saiwona nsima tsiku limenelo.
.
6- Incubator: awa ndi akazi oti ali ndi ana 3, 4, 5, 6, 7 koma sanakwatiwepo. Iwo koma kubereka ana ndi azibambo
ongodutsa basi! Mwana aliyense bambo wake!
.
7- Janasi: akazi wongodziwa ntchito zakuchipinda basi! Kuphika, kuchapa, kusamala nyumba, zonse satha. Koma mugone naye! Simutsikaponso!
.
8- Super Glue: awa ndiye okakamila mwamuna sizinaonekepons?o. Olo awasonyeze kuti sakuwafuna koma
sikukakamila kwakeko.
.
9- Plasma Screen: akatswiri okhulupilira kuonetsa mabere mumavalidwe. Amachita kumwera mankhwala kuti akulitse mabere cholinga aziliyanika poyenda.

10- Automatic Answering Machine: akazi woti mwamuna kungonena kuti akufuna awagone mmene azimaliza funsolo iwo
avula ndipo agona kale, zatsalira mwamunayo! Akuti changu pamalo!
.
11- Chokonoka: kugona naye lero mawa akuwuza kuti wamupatsa mimba!
12- Mileme: azimayi opezeka usiku okhaokha. Iwo amadzuka past 4pm ready for overnight duties. Masana simungawapeze olo patavuta bwanji!
.
13- Research Station: Awa banja siliti latha liti. Akwatiwapo ena ka 5, 6, 7 and akanakwatiwabe.? Amakhala ngati akupanga kafukufuku wa kusiyana kwa amuna.