Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi sakubwera poyera ngati adzapikisane nawo pa chisankho cha chaka chamawa.
![](https://www.faceofmalawi.com/wp-content/uploads/2018/08/muluzi.jpg)
Muluzi wakhala akugwira ntchito ndi boma m’maunduna osiyanasiyana kwa zaka zinayi potsatila m’gwilizano omwe chipani cha UDF chilli nawo ndi chipani cholamura cha DPP.