Asilikari Anayi Aku Malawi Adasowa Ku DRC

Asilikari Anayi Aku Malawi Adasowa Ku DRC

Published on November 23, 2018 at 2:11 PM by Face of Malawi

62 words • approx. 1 min read

Asilikari anayi a Malawi Defence Force adasowa pamene asilikari ena okwana asanu ndi m’modzi adaphedwa m’dziko la DRC sabata latha.

Sergeant Chancy Mwakawenga, Sergeant Boniface Noah, Corporal Geoge Salimu ndi Lance Corporal Gift sakupezeka kuchokera pa 13 November, 2018.

Wachiwiri kwa unduna wa za Chitetezo, Amos Mailos, wanena izi ku Parliament pa 23 November, 2018, Chaku m’mawa ndipo akukambirana za asilikari anayi adasowa ku DRC.

 

Subscribe to our Youtube Channel: