Mlembi Wamkulu wa timu ya Mighty Wanderers a David Kanyenda wachotsedwa pa udindo. Zambiri tikupatsirani posakhalitsapa.