Team imeneyi yanenesa kuti flames izachinyidwa zigoli 5 mumphindi 10 zoyambilira pofuna kubwezela chipongwe chomwe anyamata aflames anaichita teamyi kwao,watero head coach wawo poyankhula ndi MBNV&I mumzinda waukulu wa Blantyre.