Some business people who were operating their personal boats to ferry passengers to and from Likoma Island ati sakusangalatsidwa ndi zomwe achita aboma pokonzanso sitima ya ILALA kuti izinyamula anthu.
“ILALA imangopanga charge timitengo totchipa amwene and m’mene zateromu ndiye kuti basi ife zathu zada apapa,” wadandaula mkulu wina ndipo wawonjezera kuti: “kodi a boma wa akufuna ifeyo ndi ana athu tivutike? Tizidya chani? Ati tiwonetsana.”
No comments! Be the first commenter?