Patangodutsa masiku ochepa Pres. Joyce Banda atakhululukila bambo Maxwell Kapinga pachikondwelero choti dziko lino lakwanitsa zaka 49 lili pa ufulu wodzilamulira, bambowa dzulo akhaphidwa mpaka kuphedwa atawagwira akuba mbuzi m’khola la munthu wina m’bomali.

Omwe alanga wakubayu motere, sakudziwika mpaka pano.