Wapampando wa team ya Silver Strikers wanenetsa kuti palibe player olo m’modzi amene wachotsedwa koma kuti awapanga suspend. Izi zadza chifukwa chakhalidwe lomwe osewerawa amapanga.
“Tikungofuna tiwaphunzitse khalidwe kuti adziwe zimene akupangazo ndizolakwika,si iwowo wokha ayi,tikufufuzabe ndipo tikawapeza enaso alandilaso chilango. Player asamakhale ngati naye ndi manager ayi.” Anaonjezera choncho Dr Mwale.